Quantcast
Viewing all articles
Browse latest Browse all 3254

Malawi ndi Zambia ikuthetsa miseche kudzera mwa DJ Kachamba ndi General Kanene

Wabweranso DJ Kachamba, pano nde wabwera ndi General Kanene pomwe oyimba awiriwa anyamula mbendera ya Malawi ndi Zambia polimbana ndi mchitidwe wa mabodza mu nyimbo yatsopano Miseche. Mu nyimboyi, awiriwa akuti mchitidwe wamiseche ndi umthira kuwiri ukupititsa pansi chitukuko cha maiko oyandikanawa. Ngakhale izi zilo chomwechi, awiriwa akupempha mchitidwe oti anthu azimasukirana pakakhala kufunika kopereka […]

The post Malawi ndi Zambia ikuthetsa miseche kudzera mwa DJ Kachamba ndi General Kanene appeared first on Malawi Nyasa Times - News from Malawi about Malawi.

Viewing all articles
Browse latest Browse all 3254

Trending Articles



<script src="https://jsc.adskeeper.com/r/s/rssing.com.1596347.js" async> </script>