Kwavuta kunyumba kwa Dr Joyce Banda pomwe azukulu akakamiza mtsogoleri wa dziko lino wakaleyou kuti nayo azivala ngati woyimba Jetu komanso apite akawonere ‘show’ yake. Nyimbo za celebu wamkulu, uja okwera ndege, Jetu, zikupitilira kukhala zachikoka kwa anthu amagulu onse, kuphatikizapo ana. Pomwe president wakale Dr. Joyce Banda amacheza ndi adzukulu awo awiri dzulo, wina […]
The post Jetu wavuta! Dr. Joyce Banda akakamizidwa ndi azukulu ake kuti azivala ngati Jetu komanso apite ku ‘show’ yake appeared first on Malawi Nyasa Times - News from Malawi about Malawi.↧