Chipani cha UTM chati imfa ya Soldier Lucius Banda mnjowawa kwambiri maka pomwe chipanichi chikulirabe mtsogoleri wawo a Saulos Chilima. Lucius Banda anali mkulu okopa (Campaign Director) anthu mchipani cha UTM. Mneneri wa UTM a Felix Njawala wati ngati chipani sakudziwa kuti nkumatanino ndi momwe imfa yatengera akuluakulu ake motsogozana. Afotokoza a Njawala: “Pomwe a […]
The post ‘Kulira kwake ndiye nkumatani abale?’ Chipani cha UTM chalira kumwalira kwa Lucius Banda appeared first on Malawi Nyasa Times - News from Malawi about Malawi.↧