Wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino a Michael Usi wati ndiwokhudzidwa ndi imfa ya mkhalakale mu maimbidwe Soldier Lucius Banda. Mukalata yomwe alemba, a Usi ati akulira limodzi ndi mtsogoleri wadziko lino a Lazarus Chakwera komanso Amalawi onse. Iwo atinso banja la chipani cha UTM lataya munthu yemwe amatsogolera ntchito zokopa anthu mu chipanichi komanso […]
The post Usi ayankhulapo pa imfa ya Lucius Banda: “Ntchito za Lucius zinali zozama kotero kuti zipitilira kutumikira’ appeared first on Malawi Nyasa Times - News from Malawi about Malawi.↧