Quantcast
Channel: Entertainment | Malawi Nyasa Times - News from Malawi about Malawi
Viewing all articles
Browse latest Browse all 3234

Zachitika: Paul Banda walandira K14.5m yomwe a Malawi asonkha kuti ithandize malipiro akuchipatala

$
0
0

Oyibma Paul Banda lero walandira ndalama zokwana K14.5 miliyoni zomwe a Malawi, motsogozedwa ndi Onjezani Kenani, asonkha kuti zimuthandize kulandira chithandizo kuchipatala. Katswiri oyimbayu akudwala matenda a ipso ndipo wapatsidwa ndalama zi ku nyumba kwake kwa Chatha ku Chileka mu mzinda wa Blantyre.Mukuyankhula kwawo akuti kuthokoza kwake kukuwavuta chifukwa samayembekezera zoterezi. “Zikanakhala a Malawi timathandizana […]

The post Zachitika: Paul Banda walandira K14.5m yomwe a Malawi asonkha kuti ithandize malipiro akuchipatala appeared first on Malawi Nyasa Times - News from Malawi about Malawi.

Viewing all articles
Browse latest Browse all 3234

Trending Articles



<script src="https://jsc.adskeeper.com/r/s/rssing.com.1596347.js" async> </script>